Yeremiya 41:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Ismaele mwana wa Netaniya anatuluka mu Mizipa kukakomana nao, alinkuyenda ndi kulira misozi; ndipo panali, pamene anakomana nao, anati kwa iwo, Idzani kwa Gedaliya mwana wake wa Ahikamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Ismaele mwana wa Netaniya anatuluka m'Mizipa kukakomana nao, alinkuyenda ndi kulira misozi; ndipo panali, pamene anakomana nao, anati kwa iwo, Idzani kwa Gedaliya mwana wake wa Ahikamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono Ismaele, mwana wa Netaniya, adabwera akulira kuchokera ku Mizipa kudzakumana nawo. Atakumana nawo, adati, “Bwerani, mudzaonane ndi Gedaliya mwana wa Ahikamu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ismaeli mwana wa Netaniya anachoka ku Mizipa akulira kupita kukakumana nawo. Atakumana nawo, iye anati, “Bwerani mudzaonane ndi Gedaliya mwana wa Ahikamu.” Onani mutuwo |