Yeremiya 4:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti Yehova atero kwa anthu a Yuda ndi kwa Yerusalemu, Limani masala anu, musabzale paminga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti Yehova atero kwa anthu a Yuda ndi kwa Yerusalemu, Limani masala anu, musabzale paminga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Chauta akuuza anthu a ku Yuda ndi anthu okhala ku Yerusalemu kuti, “Limani masala anu, musabzale pakati pa minga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Zimene Yehova akunena kwa anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu ndi izi: “Limani masala anu musadzale pakati pa minga. Onani mutuwo |