Yeremiya 3:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ndinati atachita zimenezo zonse, Adzabwera kwa Ine; koma sanabwere, ndipo mphwake wonyenga, Yuda, anaona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ndinati atachita zimenezo zonse, Adzabwera kwa Ine; koma sanabwere, ndipo mphwake wonyenga, Yuda, anaona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndidaaganiza kuti atachita zonsezi, adzabwerera kwa Ine, koma sadabwerere. Tsono Yuda, mbale wake wosakhulupirika uja, adaziwona zimenezo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndinaganiza kuti atachita zonsezi, adzabwerera kwa Ine, koma sanabwerere, ndipo mlongo wake wosakhulupirika uja, Yuda, anaziona zimenezi. Onani mutuwo |