Yeremiya 3:5 - Buku Lopatulika5 Kodi adzasunga mkwiyo wake kunthawi zonse? Kodi adzakudikira mpaka chimaliziro? Taona, wanena ndi kuchita zoipa monga unatero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Kodi adzasunga mkwiyo wake kunthawi zonse? Kodi adzakudikira mpaka chimaliziro? Taona, wanena ndi kuchita zoipa monga unatero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 ‘Kodi Chauta adzandipsera mtima nthaŵi zonse? Kodi adzakwiya mpaka muyaya?’ Umu ndimo m'mene unkalankhulira. Komabe iwe udapitiriza kuchita zoipa monga momwe unkathera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 kodi mudzandikwiyira nthawi zonse? Kodi ukali wanu udzakhalabe mpaka muyaya?’ Umu ndimo mmene umayankhulira, koma umapitirizabe kuchita zoyipa monga momwe umathera.” Onani mutuwo |