Yeremiya 3:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo mvula yakanidwa, ndipo panalibe mvula ya masika; ndipo unali ndi nkhope ya mkazi wadama, unakana manyazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo mvula yakanidwa, ndipo panalibe mvula ya masika; ndipo unali ndi nkhope ya mkazi wadama, unakana manyazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nchifukwa chake Chauta adaimitsa mvula, ndi mvula yam'masika yomwe sidagwe. Komabe maonekedwe ako onse nga mkazi wachiwerewere, ndipo ulibe ndi manyazi omwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nʼchifukwa chake Yehova wayimitsa mvula, ndipo mvula ya nthawi ya masika sinagwe. Komabe uli ndi maonekedwe a mkazi wachiwerewere; ndipo sukuchita manyazi ndi pangʼono pomwe. Onani mutuwo |