Yeremiya 26:3 - Buku Lopatulika3 Kapena adzamvera, nadzatembenuka, yense kusiya njira yake yoipa; kuti ndileke choipa, chimene ndinati ndiwachitire chifukwa cha kuipa kwa ntchito zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Kapena adzamvera, nadzatembenuka, yense kusiya njira yake yoipa; kuti ndileke choipa, chimene ndinati ndiwachitire chifukwa cha kuipa kwa ntchito zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mwina mwake nkutheka kuti adzamvera, ndipo aliyense adzaleka machimo ake. Tsono ndidzaleka osaŵapatsa chilango chimene ndidaati ndiŵalange nacho, chifukwa cha ntchito zao zoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mwina mwake adzamvera, ndipo aliyense adzatembenuka kuleka njira yake yoyipa. Ndiye ine ndidzaleka osapatsa chilango chimene ndinakonzekera kuti ndiwalange nacho chifukwa cha ntchito zawo zoyipa. Onani mutuwo |