Yeremiya 22:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ndidzakupangiratu iwe opasula, yense ndi zida zake; ndipo adzadula mikungudza yako yosankhika nadzaiponya m'moto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ndidzakupangiratu iwe opasula, yense ndi zida zake; ndipo adzadula mikungudza yako yosankhika nadzaiponya m'moto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndidzatuma anthu oti adzakuwononge, aliyense ali ndi zida zake. Adzadula mikungudza yako yokoma, nadzaiponya pa moto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndidzatuma anthu oti adzakuwononge, munthu aliyense ali ndi zida zake, ndipo adzadula mikungudza yako yokongola nadzayiponya pa moto. Onani mutuwo |