Yeremiya 22:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti ngati mudzachitadi ichi pamenepo, padzalowa pa zipata za nyumba iyi mafumu okhala pa mpando wachifumu wa Davide, okwera m'magaleta ndi pa akavalo, iye, ndi atumiki ake, ndi anthu ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti ngati mudzachitadi ichi pamenepo, padzalowa pa zipata za nyumba iyi mafumu okhala pa mpando wachifumu wa Davide, okwera m'magaleta ndi pa akavalo, iye, ndi atumiki ake, ndi anthu ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndithu, ukamadzamvera mau aŵa, ndiye kuti mafumu okhala pa mpando waufumu wa Davide adzapitirirabe kumalamulira. Azidzaloŵera pa zipata izi za ku nyumba ya mfumu, atakwera pa magaleta ndi pa akavalo, iwowo pamodzi ndi atumiki ao ndi anthu ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pakuti ngati udzamvera malamulo awa, ndiye kuti mafumu onse okhala pa mpando waufumu wa Davide azidzalowabe pa zipata za nyumba yaufumu ino, atakwera magaleta ndi akavalo, iwowo pamodzi ndi nduna zawo ndi anthu awo. Onani mutuwo |