Yeremiya 2:9 - Buku Lopatulika9 Chifukwa chake ndidzatsutsananso nanu, ati Yehova, ndi ana a ana anu ndidzatsutsana nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chifukwa chake ndidzatsutsananso nanu, ati Yehova, ndi ana a ana anu ndidzatsutsana nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Tsono ndidzakuimbanibe mlandu,” akuterotu Chauta. “Ndidzaimbanso mlandu zidzukulu zanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Chifukwa chake Ine ndidzakuyimbaninso mlandu,” akutero Yehova. “Ndipo ndidzayimbanso mlandu zidzukulu zanu. Onani mutuwo |