Yeremiya 16:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele; Taonani, ndidzaletsa pano, pamaso panu masiku anu, mau akukondwerera ndi mau akusangalala, mau a mkwati ndi mau a mkwitibwi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele; Taonani, ndidzaletsa pano, pamaso panu masiku anu, mau akukondwerera ndi mau akusangalala, mau a mkwati ndi mau a mkwitibwi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele, akunena kuti, “Pa nthaŵi yanu yomwe, ndiponso pa malo omwe ano ndidzathetsa mau achisangalalo ndi achimwemwe, ndipo ndidzachotsa liwu la mkwati wamwamuna ndi la mkwati wamkazi inuyo mukuwona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pakuti Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akunena kuti, ‘Pa nthawi yanu, inu mukuona ndidzathetsa mawu achimwemwe ndi achisangalalo ndiponso mawu a mkwati ndi mkwatibwi pa malo ano.’ Onani mutuwo |