Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yeremiya 16:3 - Buku Lopatulika

3 Pakuti Yehova atero za ana aamuna ndi za ana aakazi akubadwa m'malo muno, ndi za amai anawabala iwo, ndi za atate ao anawabala iwo m'dziko muno:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Pakuti Yehova atero za ana amuna ndi za ana akazi akubadwa m'malo muno, ndi za amai anawabala iwo, ndi za atate ao anawabala iwo m'dziko muno:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ndithu kunena za ana aamuna kapena ana aakazi obadwira kuno, kapenanso za amai ao ndi atate ao amene adabereka anawo m'dziko muno,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 pakuti ana aamuna ndi ana aakazi obadwira mʼdziko muno, komanso amayi awo ndi abambo awo amene anabereka anawo mʼdziko muno,

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 16:3
6 Mawu Ofanana  

Amasiye ao andichulukira Ine kopambana mchenga wa kunyanja; ndatengera wofunkha usana afunkhire mai wao wa anyamata; ndamgwetsera dzidzidzi kuwawa mtima ndi mantha.


Usatenge mkazi, usakhale ndi ana aamuna ndi aakazi m'malo muno.


Pakuti Yehova atero, Usalowe m'nyumba ya maliro, usanke kukachita maliro ao, kapena kuwalirira; pakuti ndachotsa mtendere wanga pa anthu awa, chifundo ndi nsoni zokoma, ati Yehova.


Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele; Taonani, ndidzaletsa pano, pamaso panu masiku anu, mau akukondwerera ndi mau akusangalala, mau a mkwati ndi mau a mkwitibwi.


Chifukwa chake atero Yehova, Taona, ndidzaikira anthuwa zophunthwitsa; ndipo atate ndi ana adzakhumudwa nazo pamodzi; munthu ndi mnzake adzatayika.


Nena ndi nyumba ya Israele, Atero Ambuye Yehova, Taona, ndidzadetsa malo anga opatulika, ulemerero wa mphamvu yanu, chokonda m'maso mwanu, chimene moyo wanu ali nacho chifundo; ndipo ana anu aamuna ndi aakazi otsalira inu adzagwa ndi lupanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa