Yeremiya 16:2 - Buku Lopatulika2 Usatenge mkazi, usakhale ndi ana aamuna ndi aakazi m'malo muno. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Usatenge mkazi, usakhale ndi ana aamuna ndi aakazi m'malo muno. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Usadzakwatire, usadzabale ana aamuna kapena aakazi ku malo ano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Usadzakwatire ndi kubereka ana aamuna kapena aakazi malo ano Onani mutuwo |