Yeremiya 13:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo panali atapita masiku ambiri, kuti Yehova anati kwa ine, Uka, pita ku Yufurate, nukatenge kumeneko mpango uja, ndinakuuza iwe ukaubise kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo panali atapita masiku ambiri, kuti Yehova anati mwa ine, Uka, pita ku Yufurate, nukatenge kumeneko mpango uja, ndinakuuza iwe ukaubise kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Patapita masiku ambiri Chauta adandiwuza kuti, “Nyamuka, pita ku Yufurate, ukatenge mpango wam'chiwuno uja umene ndidaakuuza kuti ukaubise kumeneko.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Patapita masiku ambiri Yehova anandiwuzanso kuti, “Pitanso ku Yufurate ndipo ukatenge lamba amene ndinakuwuza kuti ukamubise kumeneko.” Onani mutuwo |