Yeremiya 13:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ndinanka ku Yufurate, ndikukumba, nditenga mpango m'malo m'mene ndinaubisamo; ndipo, taonani, mpango unaonongeka, wosayenera kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ndinanka ku Yufurate, ndikumba, nditenga mpango m'malo m'mene ndinaubisamo; ndipo, taonani, mpango unaonongeka, wosayenera kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ine ndidapita ku Yufurate, ndipo ndidakumba pa malo amene ndidaubisa paja, nkuutenga. Koma ndidaona kuti ndi woonongeka kotheratu, wopandanso ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Choncho ndinapita ku Yufurate kukafukula lambayo ndi kumuchotsa pamalo pamene ndinamubisa, koma nthawi imeneyi nʼkuti lambayo atawonongeka kotheratu ndipo analibenso ntchito. Onani mutuwo |