Yeremiya 13:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine nthawi yachiwiri, kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine nthawi yachiwiri, kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Chauta adandiwuzanso mau kachiŵiri kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kenaka Yehova anandiyankhulanso kachiwiri kuti, Onani mutuwo |