Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yeremiya 13:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo ndinagula mpango monga mwa mau a Yehova, ndi kuvala m'chuuno mwanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo ndinagula mpango monga mwa mau a Yehova, ndi kuvala m'chuuno mwanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Choncho ndidakagula mpango, monga momwe Chauta adaandiwuzira, ndipo ndidauvala m'chiwuno.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Choncho ndinakagula lambayo, monga momwe anandiwuzira Yehova, ndipo ndinamanga mʼchiwuno mwanga.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 13:2
8 Mawu Ofanana  

Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse, osachirikizika pa luntha lako;


Nthawi imeneyo Yehova ananena ndi Yesaya, mwana wa Amozi, nati, Muka numasule chiguduli m'chuuno mwako, nuchichotse, nuvule nsapato yako kuphazi lako. Ndipo iye anatero, nayenda maliseche, ndi wopanda nsapato.


Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine nthawi yachiwiri, kuti,


Koma iwe, wobadwa ndi munthu, tamvera ichi ndilikunena nawe; usakhale iwe wopanduka, ngati nyumba ija yopanduka; tsegula pakamwa pako, nudye chomwe ndikupatsa.


Ndipo Yohane yekhayo anali nacho chovala chake cha ubweya wangamira, ndi lamba lachikopa m'chuuno mwake; ndi chakudya chake chinali dzombe ndi uchi wakuthengo.


Muli abwenzi anga inu, ngati muzichita zimene ndikulamulani inu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa