Yeremiya 13:1 - Buku Lopatulika1 Atero Yehova kwa ine, Pita, udzigulire mpango wabafuta, nudzimangire m'chuuno mwako, usauike m'madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Atero Yehova kwa ine, Pita, udzigulire mpango wabafuta, nudzimangire m'chuuno mwako, usauike m'madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta adandiwuza kuti, “Pita ukagule mpango wa nsalu yabafuta, ukavale m'chiwuno, koma osakauviika m'madzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova anandiwuza kuti, “Pita kagule lamba wansalu yosalala ndipo ukavale mʼchiwuno mwako, koma usakamuviyike mʼmadzi.” Onani mutuwo |