Yeremiya 1:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Yehova anati kwa ine, Waona bwino pakuti Ine ndidzadikira mau anga kuwachita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Yehova anati kwa ine, Waona bwino pakuti Ine ndidzadikira mau anga kuwachita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Chauta adati, “Waona bwino. Ineyo ndikuwonetsetsa kuti zichitikedi zimene ndidanena.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Yehova anandiwuza kuti, “Waona bwino, chifukwa Ine ndikuonetsetsa kuti mawu angawa akwaniritsidwe.” Onani mutuwo |