Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yakobo 3:7 - Buku Lopatulika

7 Pakuti mtundu uliwonse wa nyama ndi wa mbalamenso, wa zokwawa, ndi wa zam'nyanja, zimazoloweretsedwa, ndipo zazoloweretsedwa ndi anthu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Pakuti mtundu uliwonse wa nyama ndi wa mbalamenso, wa zokwawa, ndi wa zam'nyanja, zimazoloweretsedwa, ndipo zazoloweretsedwa ndi anthu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Munthu angathe kuŵeta mtundu uliwonse wa nyama, wa mbalame, wa zokwaŵa, ndi wazam'nyanja, ndipo adaziŵetapodi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Mitundu yonse ya nyama, ya mbalame, ya zokwawa ndi ya zolengedwa za mʼnyanja, zikuwetedwa ndipo munthu wakhala akuziweta,

Onani mutuwo Koperani




Yakobo 3:7
4 Mawu Ofanana  

pakuti ankamangidwa kawirikawiri ndi matangadza ndi maunyolo, ndipo anamwetula maunyolo, naduladula matangadza; ndipo palibe munthu anali ndi mphamvu yakumfuya.


m'menemo munali nyama za miyendo inai za mitundu yonse, ndi zokwawa za padziko ndi mbalame za m'mlengalenga.


Ndipo lilime ndilo moto; ngati dziko la chosalungama mwa ziwalo zathu laikika lilime, ndili lodetsa thupi lonse, niliyatsa mayendedwe a chibadwidwe, ndipo liyatsidwa ndi Gehena.


koma lilime palibe munthu akhoza kulizoloweretsa; lili choipa chotakataka, lodzala ndi ululu wakupha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa