Yakobo 2:12 - Buku Lopatulika12 Lankhulani motero, ndipo chitani motero, monga anthu amene adzaweruzidwa ndi lamulo la ufulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Lankhulani motero, ndipo chitani motero, monga anthu amene adzaweruzidwa ndi lamulo la ufulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono muzilankhula ndi kuchita zinthu monga anthu oti Mulungu adzaŵaweruza potsata lamulo loŵapatsa ufulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Muziyankhula ndi kuchita zinthu monga anthu amene mudzaweruzidwe ndi lamulo limene limapereka ufulu, Onani mutuwo |