Yakobo 2:10 - Buku Lopatulika10 Pakuti aliyense amene angasunge malamulo onse, koma akakhumudwa pa limodzi, iyeyu wachimwira onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pakuti amene aliyense angasunge malamulo onse, koma akakhumudwa pa limodzi, iyeyu wachimwira onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pajatu munthu wotsata Malamulo onse, akangophonyapo ngakhale pa mfundo imodzi yokha, ndiye kuti wachimwira Malamulo onsewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pakuti amene amasunga Malamulo onse, akangophwanya fundo imodzi yokha, waphwanya Malamulo onse. Onani mutuwo |