Yakobo 1:10 - Buku Lopatulika10 ndipo mbale wolemera anyadire pamene atsitsidwa, pakuti adzapita monga duwa la udzu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 pakuti adzapita monga duwa la udzu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndipo mbale wolemera nayenso anyadire pamene Mulungu amtsitsa, pakuti adzatha ngati duŵa la udzu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Koma olemera anyadire pamene atsitsidwa, chifukwa adzatha ngati duwa lakuthengo. Onani mutuwo |