Tito 3:10 - Buku Lopatulika10 Munthu wopatukira chikhulupiriro, utamchenjeza kamodzi ndi kawiri, umkanize, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Munthu wopatukira chikhulupiriro, utamchenjeza kamodzi ndi kawiri, umkanize, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Munthu woyambitsa mipatuko, utamdzudzula kaŵiri konse, usakhale nayenso nkanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Munthu woyambitsa mipatuko umuchenjeze koyamba, ndiponso umuchenjeze kachiwiri. Kenaka umupewe. Onani mutuwo |