Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Tito 1:13 - Buku Lopatulika

13 Umboni uwu uli woona. Mwa ichi uwadzudzule mokalipa, kuti akakhale olama m'chikhulupiriro,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Umboni uwu uli woona. Mwa ichi uwadzudzule mokalipa, kuti akakhale olama m'chikhulupiriro,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Mau ameneŵa ngotsimikizika. Nchifukwa chake uŵadzudzule kwamphamvu anthuwo, kuti akhale ndi chikhulupiriro cholimba,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Mawu amenewa ndi woona. Nʼchifukwa chake, uwadzudzule mwamphamvu, kuti akhale ndi chikhulupiriro choona,

Onani mutuwo Koperani




Tito 1:13
12 Mawu Ofanana  

Mtima wanga ukhale wangwiro m'malemba anu; kuti ndisachite manyazi.


Akandipanda munthu wolungama ndidzati nchifundo: akandidzudzula, ndidzakuyesa mafuta a pamutu; mutu wanga usakane: Pakuti pangakhale posautsidwa iwo ndidzawapempherera.


Chidzudzulo chomveka chiposa chikondi chobisika.


Usamamuda mbale wako mumtima mwako; umdzudzule munthu mnzako ndithu, usadzitengera uchimo chifukwa cha iye.


Chifukwa cha ichi ndilembera izi pokhala palibe ine, kuti pokhala ndili pomwepo ndingachite mowawitsa, monga mwa ulamuliro umene Ambuye anandipatsa ine wakumangirira, ndipo si wakugwetsa.


achigololo, akuchita zoipa ndi amuna, akuba anthu, amabodza, olumbira zonama, ndipo ngati kuli kena kakutsutsana nacho chiphunzitso cholamitsa;


Ngati ukumbutsa abale zinthu izi, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu, woleredwa m'mauwo a chikhulupiriro, ndi malangizo abwino amene udawatsata;


Iwo akuchimwa uwadzudzule pamaso pa onse, kuti otsalawo achite mantha.


lalikira mau; chita nao pa nthawi yake, popanda nthawi yake; tsutsa, dzudzula, chenjeza, ndi kuleza mtima konse ndi chiphunzitso.


Izi lankhula, ndipo uchenjeze, nudzudzule ndi ulamuliro wonse. Munthu asakupeputse.


okalamba akhale odzisunga, olemekezeka, odziletsa, olama m'chikhulupiriro, m'chikondi, m'chipiriro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa