Tito 1:12 - Buku Lopatulika12 Wina wa mwa iwo, ndiye mneneri wa iwo okha, anati, Akrete ndiwo amabodza masiku onse, zilombo zoipa, aumbombo, aulesi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Wina wa mwa iwo, ndiye mneneri wa iwo okha, anati, Akrete ndiwo amabodza masiku onse, zilombo zoipa, aumbombo, aulesi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mneneri wina wa ku Krete, mmodzi mwa iwo omwewo, adati, “Akrete nthaŵi zonse ndi amabodza, zilombo zoipa, alesi adyera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mneneri wina, mmodzi wa iwo omwewo anati, “Akrete nthawi zonse ndi amabodza, akhalidwe loyipitsitsa ndiponso alesi adyera.” Onani mutuwo |