Rute 4:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Naomi anamtenga mwanayo, namuika pachifuwa pake, nakhala mlezi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Naomi anamtenga mwanayo, namuika pachifuwa pake, nakhala mlezi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Naomi adanyamula mwanayo namfukata ndipo adakhala mlezi wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kenaka Naomi anatenga mwanayo namufukata ndipo anakhala mlezi. Onani mutuwo |