Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Rute 4:17 - Buku Lopatulika

17 Ndi akazi anansi ake anamutcha dzina, ndi kuti, Kwa Naomi kwambadwira mwana; namutcha dzina lake Obedi; ndiye atate wa Yese atate wa Davide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndi akazi anansi ake anamutcha dzina, ndi kuti, Kwa Naomi kwambadwira mwana; namutcha dzina lake Obedi; ndiye atate wa Yese atate wa Davide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Akazi achinansi ake adalengeza kuti, “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Ndipo adamutcha dzina loti Obedi. Iyeyu adakhala bambo wake wa Yese, bambo wa Davide.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Amayi achinansi ake anati, “Naomi ali ndi mwana wamwamuna.” Ndipo anamutcha dzina lake Obedi. Iye anali abambo a Yese abambo ake a Davide.

Onani mutuwo Koperani




Rute 4:17
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Naomi anamtenga mwanayo, namuika pachifuwa pake, nakhala mlezi wake.


Iyo ndiyo mibadwo ya Perezi; Perezi anabala Hezironi;


ndi Obedi anabala Yese, ndi Yese anabala Davide.


Ndipo Yehova ananena ndi Samuele, Iwe ukuti ulire chifukwa cha Saulo nthawi yotani, popeza Ine ndinamkana kuti asakhale mfumu ya Israele? Dzaza nyanga yako ndi mafuta, numuke, ndidzakutumiza kwa Yese wa ku Betelehemu; pakuti ndinadzionera mfumu pakati pa ana ake.


Tsono Davide anali mwana wa Mwefurati uja wa ku Betelehemu ku Yuda, dzina lake ndiye Yese; ameneyu anali nao ana aamuna asanu ndi atatu; ndipo m'masiku a Saulo munthuyo anali nkhalamba, mwa anthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa