Rute 3:9 - Buku Lopatulika9 Nati iye, Ndiwe yani? Nayankha iye, Ndine Rute mdzakazi wanu; mufunde mdzakazi wanu chofunda chanu, pakuti inu ndinu wondiombolera cholowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Nati iye, Ndiwe yani? Nayankha iye, Ndine Rute mdzakazi wanu; mufunde mdzakazi wanu chofunda chanu, pakuti inu ndinu wondiombolera cholowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mkaziyo adayankha kuti, “Ndine Rute mdzakazi wanu. Popeza kuti ndinu wachibale, muyenera kundiwombola pakundiloŵa chokolo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iye anafunsa kuti, “Ndiwe yani?” Ndipo anayankha kuti, “Ndine mdzakazi wanu Rute. Popeza ndinu wachibale amene muyenera kundiwombola, ndiye mundilowe chokolo.” Onani mutuwo |