Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Rute 3:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo kunali, pakati pa usiku munthuyo anadzidzimuka, natembenuka; ndipo taona pa mapazi ake pagona mkazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo kunali, pakati pa usiku munthuyo anadzidzimuka, natembenuka; ndipo taona pa mapazi ake pagona mkazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tsono pakati pa usiku Bowazi adadzidzimuka natembenuka, naona mkazi atagona ku mapazi ake. Adafunsa kuti, “Ndiwe yani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Tsono pakati pa usiku Bowazi anadzidzimuka, natembenuka, ndipo anangoona mkazi akugona ku mapazi ake.

Onani mutuwo Koperani




Rute 3:8
2 Mawu Ofanana  

Ndipo atatha Bowazi kudya ndi kumwa, nusekerera mtima wake, anakagona kuthungo kwa mulu wa tirigu; nadza iye kachetechete, navundukula ku mapazi ake, nagona.


Nati iye, Ndiwe yani? Nayankha iye, Ndine Rute mdzakazi wanu; mufunde mdzakazi wanu chofunda chanu, pakuti inu ndinu wondiombolera cholowa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa