Rute 3:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo ananena naye, Zonse muzinena ndidzachita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo ananena naye, Zonse muzinena ndidzachita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Rute adayankha kuti, “Zonse mwanenazi ndichita.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Rute anayankha kuti, “Ndichita zonse zimene mwanena.” Onani mutuwo |