Rute 3:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo kudzali, akagona, upenye apo ati agone, numuke, nuvundukule ku mapazi ake, nugone, ndi iyeyo adzakufotokozera zoyenera kuchita iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo kudzali, akagona, upenye apo ati agone, numuke, nuvundukule ku mapazi ake, nugone, ndi iyeyo adzakufotokozera zoyenera kuchita iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pamene akukagona, ukaonetsetse malo amene akagonewo. Tsono ukavundukule chofunda chake nukagona ku mapazi ake. Motero iyeyo akakuuza zoti uchite.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Akamakagona, iwe ukaonetsetse malo amene wagonawo. Kenaka upite ndi kuvundukula chofunda ku mapazi ake ndi kugona. Iyeyo akakuwuza zoti uchite.” Onani mutuwo |