Rute 3:3 - Buku Lopatulika3 Usambe tsono, nudzole, nuvale zovala zako, nutsikire popunthirapo, koma usadziwike naye munthuyo, koma atatha kudya ndi kumwa ndiko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Usambe tsono, nudzole, nuvale zovala zako, nutsikire popunthirapo, koma usadziwike naye munthuyo, koma atatha kudya ndi kumwa ndiko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Samba tsono, udzole mafuta ndipo uvale zovala zabwino kwambiri, upite kopunthirako. Koma munthuyo asakakuzindikire mpaka atamaliza kudya ndi kumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Samba ndi kudzola mafuta onunkhira, ndipo uvale zovala zako zabwino kwambiri. Kenaka upite ku malo opunthirako tirigu ndi barele koma munthuyo asakakuzindikire kufikira atamaliza kudya ndi kumwa. Onani mutuwo |