Rute 3:6 - Buku Lopatulika6 Pamenepo anatsikira popunthirapo, nachita zonse monga umo mpongozi wake adamuuza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pamenepo anatsikira popunthirapo, nachita zonse monga umo mpongozi wake adamuuza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Choncho Rute adapita kopunthira kuja, ndipo adakachitadi monga momwe mpongozi wake uja adaamuuzira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho Rute anapita ku malo opunthirawo ndipo anachita monga momwe apongozi ake anamuwuza. Onani mutuwo |