Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Rute 3:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo pamene anadza kwa mpongozi wake, iye anati, Wapeza bwanji, mwana wanga? Pamenepo anamfotokozera zonse anamchitira munthuyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo pamene anadza kwa mpongozi wake, iye anati, Wapeza bwanji, mwana wanga? Pamenepo anamfotokozera zonse anamchitira munthuyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Atafika kwa mpongozi wake uja, mpongoziyo adati, “Zinthu zakuyendera bwanji, mwana wanga?” Rute adamfotokozera zonse zimene munthu uja adamchitira,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Rute atafika kwa apongozi ake anamufunsa kuti, “Zinayenda bwanji mwana wanga?” Kenaka iye anafotokoza zonse zimene Bowazi anamuchitira.

Onani mutuwo Koperani




Rute 3:16
2 Mawu Ofanana  

Ndipo anati, Bwera nacho chofunda chako, nuchigwire; nachigwira iye; ndipo anayesa miyeso isanu ndi umodzi ya barele, namsenza; atatero analowa m'mzinda.


Natinso, Miyeso iyi isanu ndi umodzi ya barele anandipatsa, pakuti anati, Usafike kwa mpongozi wako wopanda kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa