Rute 3:17 - Buku Lopatulika17 Natinso, Miyeso iyi isanu ndi umodzi ya barele anandipatsa, pakuti anati, Usafike kwa mpongozi wako wopanda kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Natinso, Miyeso, iyi isanu ndi umodzi ya barele anandipatsa, pakuti anati, Usafike kwa mpongozi wako wopanda kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 ndipo adati, “Wandipatsa makilogramu makumi aŵiri a barele, nandiwuza kuti, ‘Usapite kwa apongozi ako chimanjamanja.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ndipo anati, “Munthuyo anandipatsa makilogalamu makumi awiri awa a barele, nandiwuza kuti usapite kwa apongozi ako wopanda kanthu.” Onani mutuwo |