Rute 3:1 - Buku Lopatulika1 Pamenepo Naomi mpongozi wake ananena naye, Mwana wanga, kodi ndisakufunire popumulako, kuti ukhale bwino? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamenepo Naomi mpongozi wake ananena naye, Mwana wanga, kodi ndisakufunire popumulako, kuti ukhale bwino? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina Naomi adafunsa Rute kuti, “Kodi iwe mwana wanga, nanga sikwabwino kuti ndikupezere pokhala, kuti zinthu zizikuyendera bwino? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsiku lina Naomi anafunsa mpongozi wake Rute kuti, “Mwana wanga, kodi si kwabwino kuti ndikupezere kokhala kuti zinthu zizikuyendera bwino? Onani mutuwo |