Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Rute 1:9 - Buku Lopatulika

9 Yehova akuloleni mupeze mpumulo yense m'nyumba ya mwamuna wake. Nawapsompsona, nakweza iwo mau ao nalira misozi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Yehova akuloleni mupeze mpumulo yense m'nyumba ya mwamuna wake. Nawapsompsona, nakweza iwo mau ao nalira misozi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Chauta akuthandizeni kuti mupeze pokhala, ndipo aliyense mwa inu akwatiwe.” Pompo adaŵampsompsona. Koma iwo adayamba kulira mokweza,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 “Yehova akuthandizeni kuti aliyense wa inu apeze pokhala pabwino komanso mwamuna.” Kenaka anawapsompsona koma awiriwo analira mokweza.

Onani mutuwo Koperani




Rute 1:9
8 Mawu Ofanana  

Ndipo anasendera nampsompsona; ndipo anamva kununkhira kwa zovala zake, namdalitsa, nati, Taona, kununkhira kwa mwana wanga, kufanana ndi kununkhira kwa munda anaudalitsa Yehova;


Ndipo Yakobo anampsompsona Rakele nakweza mau ake, nalira.


Ndipo sunandiloleze ine ndimpsompsone ana anga aamuna ndi aakazi? Wapusa iwe pakuchita chotero.


Ndipo anampsompsona abale ake onse, nalirira iwo; ndipo pambuyo pake abale ake onse anacheza naye.


Ndipo onsewa analira kwambiri, namkupatira Paulo pakhosi pake, nampsompsona,


Ndipo ananena naye, Iai, koma tidzapita nanu kwa anthu a kwanu.


Ndipo Naomi anati kwa apongozi ake awiri, Mukani, bwererani yense wa inu kunyumba ya amai wake; Yehova akuchitireni zokoma, monga umo munachitira akufa aja ndi ine.


Pamenepo Naomi mpongozi wake ananena naye, Mwana wanga, kodi ndisakufunire popumulako, kuti ukhale bwino?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa