Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Obadiya 1:2 - Buku Lopatulika

2 Taona, ndakuika wamng'ono mwa amitundu; unyozedwa kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Taona, ndakuika wamng'ono mwa amitundu; unyozedwa kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Chauta akuuza Aedomu kuti, “Ndithu ndidzakutsitsani kotheratu, anthu a mitundu yonse adzakunyozani kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Taona, ndidzakuchepetsani pakati pa anthu a mitundu ina; udzanyozedwa kwambiri.

Onani mutuwo Koperani




Obadiya 1:2
9 Mawu Ofanana  

Yehova wa makamu wapanga uphungu uwu, kuipitsa kunyada kwa ulemerero wonse, kupepula onse olemekezeka a m'dziko lapansi.


Pakuti, taona, ndakuyesa iwe wamng'ono mwa amitundu, ndi wonyozedwa mwa anthu.


Udzakhala wopepuka wa maufumu onse, sudzadzikwezanso pa amitundu; ndipo ndidzawachepsa, kuti asachitenso ufumu pa amitundu.


Pamenepo mdani wanga adzachiona, ndi manyazi adzamkuta iye amene adati kwa ine, Ali kuti Yehova Mulungu wako? Maso anga adzamuona; tsopano adzampondereza ngati thope la m'miseu.


Ndi Edomu adzakhala akeake, Seiri lomwe lidzakhala lakelake, ndiwo adani ake; koma Israele adzachita zamphamvu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa