Obadiya 1:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo nyumba ya Yakobo idzakhala moto, ndi nyumba ya Yosefe lawi, ndi nyumba ya Esau ngati chiputu, ndipo adzawatentha pakati pao, ndi kuwapsereza; ndipo sadzakhalapo otsalira nyumba ya Esau; pakuti Yehova wanena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo nyumba ya Yakobo idzakhala moto, ndi nyumba ya Yosefe lawi, ndi nyumba ya Esau ngati chiputu, ndipo adzawatentha pakati pao, ndi kuwapsereza; ndipo sadzakhalapo otsalira nyumba ya Esau; pakuti Yehova wanena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Fuko la Yakobe lidzakhala ngati moto, fuko la Yosefe lidzakhala ngati malaŵi a moto, fuko la Esau lidzakhala ngati ziputu. Adzaŵatentha ndi kuŵapsereza, ndipo sipadzapulumuka munthu aliyense.” Akutero Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Nyumba ya Yakobo idzasanduka moto ndipo nyumba ya Yosefe idzasanduka lawi la moto; nyumba ya Esau idzasanduka chiputu, ndipo adzayitenthe pa moto ndi kuyipsereza. Sipadzakhala anthu opulumuka kuchokera mʼnyumba ya Esau.” Yehova wayankhula. Onani mutuwo |