Numeri 9:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo pakukhalitsa mtambo masiku ambiri pamwamba pa chihema, pamenepo ana a Israele anasunga udikiro wa Yehova osayenda ulendo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo pakukhalitsa mtambo masiku ambiri pamwamba pa Kachisi, pamenepo ana a Israele anasunga udikiro wa Yehova osayenda ulendo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ngakhale mtambowo ukhale masiku ambiri pamwamba pa chihemacho, Aisraele ankasungabe lamulo la Chauta, ndipo sankanyamuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mtambowo ukakhala pa chihema nthawi yayitali, Aisraeli ankasungabe lamulo la Yehova ndipo iwo sankasamukanso. Onani mutuwo |