Numeri 8:25 - Buku Lopatulika25 ndipo kuyambira zaka makumi asanu azileka kutumikira utumikiwu, osachitanso ntchitoyi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 ndipo kuyambira zaka makumi asanu azileka kutumikira utumikiwu, osachitanso ntchitoyi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Akafika zaka makumi asanu aleke ntchito yotumikira, ndipo asatumikirenso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Koma akakwana zaka makumi asanu, apume pa ntchito yawo ya tsiku ndi tsiku ndi kulekeratu kugwira ntchitoyo. Onani mutuwo |