Numeri 8:24 - Buku Lopatulika24 Ichi ndi cha Alevi: kuyambira ali wa zaka makumi awiri ndi zisanu ndi mphambu azilowa kutumikira utumikiwu mu ntchito ya chihema chokomanako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ichi ndi cha Alevi: kuyambira ali wa zaka makumi awiri ndi zisanu ndi mphambu azilowa kutumikira utumikiwu mu ntchito ya chihema chokomanako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 “Ntchito za Alevi ndi izi: kuyambira anthu a zaka 25 ndi opitirirapo, azipita kukagwira ntchito yotumikira m'chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Ntchito za Alevi ndi izi: Amuna a zaka 24 kapena kuposera pamenepa ndiye azibwera kudzagwira ntchito ku tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |