Numeri 8:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo ndatenga Alevi m'malo mwa oyamba kubadwa onse mwa ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo ndatenga Alevi m'malo mwa oyamba kubadwa onse mwa ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono pakati pa Aisraele ndaŵatenga Alevi m'malo mwa ana onse oyamba kubadwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndipo ndatenga Alevi mʼmalo mwa ana aamuna onse oyamba kubadwa mu Israeli. Onani mutuwo |