Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 8:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ndipo ndatenga Alevi mʼmalo mwa ana aamuna onse oyamba kubadwa mu Israeli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 Ndipo ndatenga Alevi m'malo mwa oyamba kubadwa onse mwa ana a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo ndatenga Alevi m'malo mwa oyamba kubadwa onse mwa ana a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Tsono pakati pa Aisraele ndaŵatenga Alevi m'malo mwa ana onse oyamba kubadwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 8:18
5 Mawu Ofanana  

Koma Israeli anapinganitsa mikono motero kuti anayika dzanja lake lamanja pamutu pa Efereimu ngakhale kuti iyeyo anali wamngʼono ndi dzanja lake lakumanzere analisanjika pamutu pa Manase ngakhale kuti iyeyu ndiye anali mwana woyamba.


“Pakati pa Aisraeli onse ndatenga Alevi kulowa mʼmalo mwa mwana wamwamuna aliyense woyamba kubadwa kwa amayi a Chiisraeli. Alevi ndi anga,


Pereka Alevi kwa Aaroni ndi kwa ana ake aamuna. Amenewa ndiwo Aisraeli amene aperekedwa kwa iye kwathunthu.


Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa mu Israeli, kaya wa munthu kapena wa ziweto, ndi wanga. Pamene ndinakantha ana oyamba kubadwa ku Igupto, ndinawapatulira kwa Ine mwini.


Mwa Aisraeli onse, ndapereka Alevi kuti akhale mphatso kwa Aaroni ndi ana ake aamuna kugwira ntchito ya ku tenti ya msonkhano mʼmalo mwa Aisraeli onse kuti azikapereka nsembe yopepesera machimo, kuti mliri usadzaphe Aisraeli pamene ayandikira ku malo wopatulika.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa