Numeri 7:9 - Buku Lopatulika9 Koma sanapatse ana a Kohati kanthu; popeza ntchito yao ndiyo ya zinthu zopatulika, zimene amazisenza pa mapewa ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma sanapatse ana a Kohati kanthu; popeza ntchito yao ndiyo ya zinthu zopatulika, zimene amazisenza pa mapewa ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma ana a Kohati sadaŵapatse kanthu, chifukwa iwowo anali ndi ntchito yosamala zinthu zoyera zimene ankanyamulira pa phewa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma Mose sanapereke zimenezi kwa Akohati chifukwa zinthu zawo zopatulika zomwe ankayangʼanira zinali zoti azinyamula pa mapewa awo. Onani mutuwo |