Numeri 7:87 - Buku Lopatulika87 ng'ombe zonse za nsembe yopsereza ndizo ng'ombe khumi ndi ziwiri, nkhosa zamphongo khumi ndi ziwiri, anaankhosa a chaka chimodzi khumi ndi awiri, pamodzi ndi nsembe yao yaufa; ndi atonde a nsembe zauchimo khumi ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201487 ng'ombe zonse za nsembe yopsereza ndizo ng'ombe khumi ndi ziwiri, nkhosa zamphongo khumi ndi ziwiri, anaankhosa a chaka chimodzi khumi ndi awiri, pamodzi ndi nsembe yao yaufa; ndi atonde a nsembe zauchimo khumi ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa87 Nyama zonse zoperekera nsembe zopsereza zinali ng'ombe zamphongo khumi ndi ziŵiri, nkhosa zamphongo khumi ndi ziŵiri, anaankhosa amphongo a chaka chimodzi khumi ndi aŵiri, pamodzi ndi chopereka cha chakudya, ndiponso atonde khumi ndi aŵiri operekera nsembe zopepesera machimo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero87 Chiwerengero cha nyama zonse za nsembe yopsereza chinali motere: ngʼombe zazimuna khumi ndi ziwiri, nkhosa zazimuna khumi ndi ziwiri ndi ana ankhosa aamuna khumi ndi awiri a chaka chimodzi pamodzi ndi chopereka chachakudya. Mbuzi zazimuna khumi ndi ziwiri zinali za nsembe yopepesera machimo. Onani mutuwo |