Numeri 7:86 - Buku Lopatulika86 Zipande zagolide ndizo khumi ndi ziwiri, zodzala ndi chofukiza, chipande chonse masekeli khumi, kuyesa sekeli wa malo opatulika; golide wonse wa zipandezo ndiwo masekeli zana limodzi ndi makumi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201486 Zipande zagolide ndizo khumi ndi ziwiri, zodzala ndi chofukiza, chipande chonse masekeli khumi, kuyesa sekeli wa malo opatulika; golide wonse wa zipandezo ndiwo masekeli zana limodzi ndi makumi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa86 Timbale khumi ndi tiŵiri tagolide todzaza ndi lubani timene tinkalemera kalikonse magaramu 110, potsata muyeso wa ku malo opatulika, tonse pamodzi tinkalemera ngati kilogaramu limodzi ndi theka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero86 Mbale khumi ndi ziwiri zagolide zodzaza ndi lubanizo zinkalemera magalamu 110 iliyonse, monga mwa muyeso wa ku malo opatulika. Pamodzi, mbale zagolide zinkalemera kilogalamu imodzi ndi theka. Onani mutuwo |