Numeri 7:80 - Buku Lopatulika80 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201480 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa80 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzadza ndi lubani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero80 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; Onani mutuwo |