Numeri 7:80 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero80 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; Onani mutuwoBuku Lopatulika80 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201480 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa80 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzadza ndi lubani, Onani mutuwo |