Numeri 7:78 - Buku Lopatulika78 Tsiku lakhumi ndi chiwiri kalonga wa ana a Nafutali, ndiye Ahira mwana wa Enani: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201478 Tsiku lakhumi ndi chiwiri kalonga wa ana a Nafutali, ndiye Ahira mwana wa Enani: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa78 Tsiku la 12 linali la Ahira mwana wa Enani, mtsogoleri wa Anafutali, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero78 Pa tsiku la khumi ndi chimodzi Ahira mwana wa Enani, mtsogoleri wa fuko la Nafutali, anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |